Untold Stories: The woman on TV

Akule

I swear on this day I did not want to go out for a drink, no! I wanted to be home, watch TV while taking a glass of Sobo, chete. I had just came back from the village where I visited some relatives. A trip to the village is exciting, full of memories and stories.

Something interesting happened in the village. We had finished the day and everyone went to sleep. I said a little prayer and slept pa mphatsa yomwe anandiyalira pa balaza mu nyumba ya auntie anga. I was sleeping peacefully when I noticed kuti tinthu tinatake tikundiluma komanso kundiendaenda. I switched on my fon, eeeeeh! chofunda chonse nyerere zokhazokha, I immediately screamed!

“Achimwene ndichani?” my auntie asked. I said nyerere zikundisowetsa mtendere kuno, mumagonamo bwanji muno? My auntie just laughed “aaaaa! ndie mpaka kukuwa choncho … ifetu tinazolowera.” I did not say anything, I just went out of the house and slept in the car till morning. “Pali ndi zinthu zake zozolowera osati zimenezi, masewera eti” ndinazilankhulira ndekhandekha.

I swear on this day I did not want to go out for a drink. So I was at home watching TV with my wife while telling her about what I experienced on my trip to the village. Amamvetsera ndi chidwi ine ndikufotokoza nkhaniyi, kenaka mwadzidzidzi I stopped explaining. She asked me “ndie kutacha zinatha bwanji?” Ineyo funsolo sindinalimve nkomwe, all my attention was on the advert about a new toothpaste that was playing on the TV.

She shouted “eeeeeh! Akule ndie zinatha bwanji? Ine nkudzidzimuka koma nditaiwala kuti timakamba nkhani yanji. I innocently asked “kodi timakamba nkhani yanji paja?” … “Nkazi wapa TV yo mpaka kumuyang’ana choncho … mpakana kukuiwalitsani nkhani mmmhuuu!” she said. There was a woman on the TV, Yes! the woman in the advert. To be honest she was everything that fits the definition of a beautiful woman.

This angelically looking woman was dark in complexion like chocolate colour, she had pure white teeth, the clothes she wore ngati anachita kusokera mthupi momwemo, anali ndi ma dimples ngati akupangira dala, komanso kachipumi kopanda masweswe. Her smile can make you feel cold on a sunny day and feel hot on a cold day. She was simply beautiful, a perfect person to advertise the new toothpaste.

My wife thought I was disturbed by the looks of the woman on TV, hahahahaha! sanadziwe kuti chidwi changa chonse chinali poti ndimve dzina la toothpaste wasopanoyi. I swear I did not want to go out for a drink, nanga tizikangana za munthu wapa TV hahahaha!

%d bloggers like this: