Untold Stories: DNA Test

By: Akule Chikopa

Simply put a DNA test also known as genetic test is a test done by gynecologists to identify someone or to show that people are related. One of my favorite TV shows is Laurine Lake’s “Paternity Court.” In this court there are no battles over issues of money, rents, loans, damages, no! They only deal with emotional cases solved by DNA tests.

In Paternity Court they normally contest on issues to do with whether someone is really a father of a child or not. In these advanced countries munthu akakana mimba kapena iyeyo akukaikira kuti mwanayo siwake, nkhani zimenezi zimakathera ku partenity court. So on that TV show I have seen people in relationships shading tears of pain or happiness. I have seen relationships and marriages being destroyed or being built because of DNA tests.

Now from a snap chart and the little knowledge that I have on DNA tests in Malawi, I have come to realise that “DNA test ndiyodula kwambiri” it is very expensive. This means most Malawians cannot afford to go for it. By the way, ku Malawi kunonso sizidziwika bwinobwino kuti DNA test amapangadi or chipatala chimene amapanga zimenezi sichidziwikanso.

Surely, takhala tikunamizana nthawi yaitali a Malawi pankhani imeneyi. Our brothers akanako mimba zoti ndizawo ndithu komanso our innocent brothers akulera ana oti siawo mmakomomu. Lord have mercy! Our innocent sisters akanidwapo ndi munthu woti mimba ndiyake ndithu komanso our evil sisters amupachikapo munthu woti mimba siyake ndithu. Kungomupezelera ndi kumupaka munthu mimba, Hahahaha! Ndikuseka ngati zabwino.

Reaching this far, I strongly feel we need paternity courts and DNA testing centres mu dziko lathu lino. Hahahahaha! Komatu kutha kukhala chipasupasu! You see tanamizana kokwanira a Malawi. M’bambo akangopita kokaona mwana woti wabadwa kumene kuchipatala azimayi amakhala ndi njira zawo zoti iweyo usakaikirenso kuti mwanayo ndiwako. Umva “uyu ndiye wakutengani chilichonse uyu, taonani ka mphuno kakeko… mungomupatsa dzina loti junior” hahahaha! Pamenepo ungalimbenso.

Azimayi ndiochenjeratu kwambiri, umva “uyu, uyu yekha ndiye sanatengele kwanu bamboo … uyuyu akufanana ndi agogo ake akuchikazi … mwaliona phazili ndendende la agogo ake” hahahaha! Yatha nkhani ikatero, nanga iweyo mpata woti ukafananize mapazi siwungaupeze, mwinanso amatchula kuti mwanayo akufanana ndi munthu woti anamwalira kalekale. This is what we have been going through, kunamizana basi.

Nkhani ya mimba ikafika kwa a mfumu ndiye imangolakwiratu munthu wa mamuna chako palibe. Amakufunsa funso limodzi “Achimwene mtsikanayu mukumudziwa?” Iwe ukangoyankha kuti “eya ndikumudziwa,” nkhani yathera pomwepo. Hahahaha! Zilimo m’makomoku ana kukhala nawo bwinobwino koma m’modzi yekha ukamuyang’ana zochitika zake, kumuona ka shape kamutu, ka nkhongo kosiyana ndi abale ake onse, zokaikitsa zija ndithu. Ukati udandaule kuti koma mwana uyu kuyela kumeneku anatengera ndani, tsitsi ngati n’kaladi chonchi umangomva “m’mimmba ndi m’chipalatu paja, muzithokoza Mulungu inu mwana ndi mphatso.

DNA test …chipasupasu chifike, a Malawi tanamizana kwakwana.

 

%d bloggers like this: